Face To Face - Chichewa Edition
F. Wayne Mac Leod
Broschiertes Buch

Face To Face - Chichewa Edition

Kuyang'ana Mwa Uzimu Pa Moyo Wa Mose, Munthu Amene Mulungu Adamuona Maso Ndi Maso

Versandkostenfrei!
Versandfertig in 1-2 Wochen
8,99 €
inkl. MwSt.
PAYBACK Punkte
4 °P sammeln!
MASO NDI MASOKuyang'ana Mwa Uzimu Pa Moyo Wa Mose, Munthu Amene Mulungu Adamuona Maso Ndi Maso Panalibe mwamuna kapena mkazi amene anayenda pafupi ndi Mulungu monga Mose anachitira. Apa panali munthu amene anakhala masiku pamaso pa Mulungu. Analankhula ndi Mulungu maso ndi maso monga mmene timalankhulira ndi mnzathu. Moyo wake unali wodzala ndi umboni wozizwitsa wa kukhalapo kwa Mulungu. Kodi iye anali munthu wotani? Anali munthu ngati inu ndi ine. Iye anali kutali ndi ungwiro. Anavutika ndi nyengo zofooketsa m'moyo. Nthawi zambiri ankakayikira ngati iyeyo ndi amene ankagwira ntchitoyo. Sikuti...