2,99 €
2,99 €
inkl. MwSt.
Sofort per Download lieferbar
payback
0 °P sammeln
2,99 €
2,99 €
inkl. MwSt.
Sofort per Download lieferbar

Alle Infos zum eBook verschenken
payback
0 °P sammeln
Als Download kaufen
2,99 €
inkl. MwSt.
Sofort per Download lieferbar
payback
0 °P sammeln
Jetzt verschenken
2,99 €
inkl. MwSt.
Sofort per Download lieferbar

Alle Infos zum eBook verschenken
payback
0 °P sammeln
  • Format: ePub

Mutu waukulu wa bukuli ndi "kubadwa mwatsopano mwa Madzi ndi Mzimu Woyera." Ili ndi chiyambi chake pa mutuwu. Mwanjira ina, bukuli limatiwuza momveka bwino chomwe kubadwa mwatsopano kuli ndi mmene tingabadwire mwatsopano mwa madzi ndi Mzimu Woyera molingana ndi Baibulo. Madzi amaimira ubatizo wa Yesu ku Yordano ndipo Baibulo limati machimo athu onse anaperekedwa kwa Yesu pamene Iye anabatizidwa ndi Yohane Mbatizi. Yohane anali woimira anthu onse ndiponso mdzukulu wa Aroni, Wansembe Wamkulu. Aroni anasanjika manja ake pamutu pa mbuzi yopereka nsembe ndipo anapititsira machimo onse a chaka cha…mehr

  • Geräte: eReader
  • mit Kopierschutz
  • eBook Hilfe
  • Größe: 0.86MB
  • FamilySharing(5)
Produktbeschreibung
Mutu waukulu wa bukuli ndi "kubadwa mwatsopano mwa Madzi ndi Mzimu Woyera." Ili ndi chiyambi chake pa mutuwu. Mwanjira ina, bukuli limatiwuza momveka bwino chomwe kubadwa mwatsopano kuli ndi mmene tingabadwire mwatsopano mwa madzi ndi Mzimu Woyera molingana ndi Baibulo. Madzi amaimira ubatizo wa Yesu ku Yordano ndipo Baibulo limati machimo athu onse anaperekedwa kwa Yesu pamene Iye anabatizidwa ndi Yohane Mbatizi. Yohane anali woimira anthu onse ndiponso mdzukulu wa Aroni, Wansembe Wamkulu. Aroni anasanjika manja ake pamutu pa mbuzi yopereka nsembe ndipo anapititsira machimo onse a chaka cha Aisraeli pa iyo pa Tsiku la Chiyanjanitso. Ichi ndi chithunzithunzi cha zinthu zabwino zikubwera. Ubatizo wa Yesu ndi chifaniziro cha kusanjika manja. Yesu anabatizidwa m'njira ya kusanjika manja ku Yordano. Choncho Iye anachotsa machimo onse a dziko lapansi kudzera mu ubatizo Wake ndipo anapachikidwa kuti alipire machimowo. Koma Akhristu ambiri sadziwa chifukwa chake Yesu anabatizidwa ndi Yohane Mbatizi mu Yordano. Ubatizo wa Yesu ndi mawu ofunika kwambiri a bukuli ndiponso gawo losatheka kuchotsa la Uthenga Wabwino wa Madzi ndi Mzimu Woyera. Tikhoza kubadwa mwatsopano pokhapokha titakhulupirira mu ubatizo wa Yesu ndi Mtanda Wake.


Dieser Download kann aus rechtlichen Gründen nur mit Rechnungsadresse in A, B, CY, CZ, D, DK, EW, E, FIN, F, GR, H, IRL, I, LT, L, LR, M, NL, PL, P, R, S, SLO, SK ausgeliefert werden.